Genesis 45:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anati kwa abale ace, Ine ndine Yosefe; kodi-akali ndi moyo atate wanga? Ndipo abale ace sanakhoza kumyankha iye; pakuti anabvutidwa pakumuona iye.

Genesis 45

Genesis 45:1-6