Genesis 44:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ife tinati kwa mbuyanga, Mnyamata sangathei kumsiya atate wace; pakuti akamsiya atate wace, atate wace adzafa.

Genesis 44

Genesis 44:15-30