Genesis 43:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yuda ananena ndi iye kuti, Munthu uja anatilimbitsira mau kuti, Simudzaonanso nkhope yanga, koma mphwanu akhale ndi inu ndiko.

Genesis 43

Genesis 43:2-11