Genesis 43:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anatucula maso ace naona Benjamini mphwace, mwana wa amace, nati, Kodi uyu ndi mphwanu wamng'ono uja, amene munanena ndi ine uja? Ndipo iye anati, Mulungu akucitire we ufulu, mwana wanga.

Genesis 43

Genesis 43:26-34