Genesis 43:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anaona Benjamini pamodzi nao, anati kwa tsanyumba wace, Lowa nao anthuwo m'nyumba, kaphere iwo, kakoozere, cifukwa anthuwo adzadya ndi ine usana uno.

Genesis 43

Genesis 43:15-18