Genesis 43:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo njala inakula m'dzikomo. Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Aigupto atate wao anati