Genesis 42:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rubeni anayankha nati kwa iwo, Kodi sindinanena kwa inu kuti, Musacimwire mwanayu; ndipo inu munakana kumvera? cifukwa cacenso, taonani mwazi wace ufunidwa.

Genesis 42

Genesis 42:15-25