Genesis 42:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tumizani mmodzi wa inu akatenge, adze naye mphwanu: ndipo inu mudzamangidwa kuti mau anu ayesedwe, ngati zoona ziri mwa inu: penatu, pali moyo wa Farao, muli ozonda ndithu.

Genesis 42

Genesis 42:7-19