Genesis 41:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kwa Yosefe anabadwa ana amuna awiri, cisanafike caka ca njala, amene Asenati mwana wamkazi wa Porifera wansembe wa Oni anambalira iye.

Genesis 41

Genesis 41:45-56