Genesis 40:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akali masiku atatu Farao adzakweza mutu wako ndi kuucotsa, nadzakupacika iwe pamtengo: ndipo mbalame zidzadya mnofu wako.

Genesis 40

Genesis 40:14-23