Genesis 4:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso kwa Seti, kwa iye kunabadwamwana wamwamuna: anamucha dzina lace Enosi: pomwepo anthu anayamba kuchula dzina la Yehova.

Genesis 4

Genesis 4:18-26