Genesis 39:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena kwa iye monga mau awa, nati, Analowa kwa ine kapolo wa Cihebri uja, munabwera naye kwathu, kundipunza ine:

Genesis 39

Genesis 39:7-20