Genesis 39:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kupfuula, iye anasiya copfunda cace kwa me nathawira kubwalo.

Genesis 39

Genesis 39:14-22