Genesis 38:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yuda anati kwa Onani, Lowani naye mkazi wa mbale wako, ndi kumcitira mkazi zoyenera mphwace wa mwamuna wace, ndi kumuukitsira mkuru wako mbeu.

Genesis 38

Genesis 38:1-16