Genesis 38:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yuda anabvomereza nati, Akhale wolungama wopambana ine, cifukwa ine sindinampatsa iye Sela mwana wanga wamwamuna. Ndipo iye sanamdziwanso mkaziyo.

Genesis 38

Genesis 38:22-30