Genesis 37:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti taonani, ndinalinkumanga mitolo m'munda, ndipo taonani, mtolo wanga unauka nuima ciriri! ndipo taonani, mitolo yanu inadza niuzinga kwete, niuweramira mtolo wanga.

Genesis 37

Genesis 37:2-13