Genesis 37:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana pita pamenepo Amidyani a malonda: ndipo anamturutsa namkweza Yosefem'dzenjemo, namgulitsa kwa Aismayeli ndi ndalama zasiliva makumi awiri; ndipo ananka naye Yosefe ku Aigupto.

Genesis 37

Genesis 37:26-31