Genesis 36:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mfumu Magidieli, mfumu Iramu; amenewa ndi mafumu a Edomu, monga mwa kukhala kwao m'dziko lokhala laolao. Uyo ndiye Esau atate wao wa Aedomu.

Genesis 36

Genesis 36:42-43