Genesis 36:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewa ndi ana amuna a Oholibama mkazi wace wa Esau; mfumu Jeusi, mfumu Jalamu, mfumu Kora, amenewa ndi mafumu obadwa kwa Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mkazi wace wa Esau.

Genesis 36

Genesis 36:13-26