Genesis 36:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amenewa ndi maina a ana amuna a Esau: Elifazi mwana wamwamuna wa Ada, mkazi wace wa Esau, Reueli mwana wamwamuna wa Basemati mkazi wace wa Esau.

Genesis 36

Genesis 36:4-19