Genesis 35:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamanga kumeneko guwa la nsembe, Dacha pamenepo El Beteli: pakuti kumeneko Mulungu anaonekera kwa iye muja anathawa pa nkhope ya mbale wace.

Genesis 35

Genesis 35:6-12