Genesis 35:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake anatsirizika nafa, nasonkhanitsidwa kwa anthu a mtundu wace, wokalamba ndi wa masiku okwanira: ndipo Esau ndi Yakobo ana ace amuna anamuika iye.

Genesis 35

Genesis 35:21-29