Genesis 35:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ana amuna a Zilipa mdzakazi wace wa Leya: ndiwo Gadi ndi Aseri: amenewo ndi ana amuna a Yakobo amene anabala iye m'Padanaramu.

Genesis 35

Genesis 35:19-29