Genesis 35:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene anabvutidwa, namwino anati kwa iye, Usaope: pakuti udzakhala ndi mwana wina wamwamuna.

Genesis 35

Genesis 35:15-25