Genesis 34:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse amene anaturuka pa cipata ca mudzi wao anamvera Hamori ndi mwana wace Sekemu, nadulidwa amuna onse akuturuka pa cipata ca mudzi wao.

Genesis 34

Genesis 34:15-25