Genesis 33:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatukula maso ace nawaona akazi ndi ana; nati, Ndani awa ali ndi iwe? Ndipo iye anati, Ndiwo ana amene Mulungu anakomera mtima kumpatsa kapolo wanu.

Genesis 33

Genesis 33:2-14