Genesis 33:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anatukula maso ace, taonani, anadza Esau, ndi pamodzi naye anthu mazana anai. Ndipo anagawira ana kwa Leya, ndi kwa Rakele, ndi kwa adzakazi awiri aja.

Genesis 33

Genesis 33:1-8