Genesis 32:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anati, Mulungu wa atate wanga Abrahamu, Mulungu wa atate wanga Isake, Yehova, amene munati kwa ine, Bwera ku dziko lako, ndi kwa abale ako, ndipo ndidzakucitira iwe bwino:

Genesis 32

Genesis 32:3-17