Genesis 32:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anaona kuti sanamlaka, anakhudza nsukunyu ya ncafu yace; ndipo nsukunyu ya ncafu yace ya Yakobo inaguluka, pakulimbana naye.

Genesis 32

Genesis 32:19-29