Genesis 32:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mundipulumutsetu ine m'dzanja la mkuru wanga, m'dzanja la Esau; cifukwa ine ndimuopa iye, kapena adzadza kudzandikantha ine, ndi amai pamodzi ndi ana.

Genesis 32

Genesis 32:1-14