Genesis 31:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'dzanja langa muli mphamvu yakucitira iwe zoipa koma Mulungu wa atate wako anati kwa ine usiku walero, kuti, Tadziyang'anira wekha, usanene kwa Yakobo kapena zabwino kapena zoipa.

Genesis 31

Genesis 31:20-30