Genesis 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuingitsa munthuyo; nakhazika Makerubi ca kum'mawa kwace kwa munda wa Edene, ndi lupanga lamoto lakuzungulira ponsepo, lakusunga njira ya ku mtengo wa moyo.

Genesis 3

Genesis 3:15-24