Genesis 3:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwamuna anamucha dzina la mkazi wace, Hava; cifukwa ndiye amace wa amoyo onse.

Genesis 3

Genesis 3:18-22