Genesis 29:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anamtumikira zaka zisanu ndi ziwiri cifukwa ca Rakele; koma zidamuonekera iye ngati masiku owerengeka cifukwa ca cikondi cimene anamkonda iye naco.

Genesis 29

Genesis 29:11-30