Genesis 29:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayang'ana, taonani, citsime m'dambo, ndipo, taonani, magulu atatu a nkhosa alinkugona kumeneko: pakuti pacitsimepo anamwetsa nkhosa; ndipo mwala wa pakamwa pa citsime unali waukuru.

Genesis 29

Genesis 29:1-5