Genesis 27:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Usendere nayo kwa ine, ndidye nyama ya mwana wanga, kuti moyo wanga ukudalitse iwe. Ndipo anasendera nayo kwa iye, nadya iye; ndipo anamtengera vinyo, namwa iye.

Genesis 27

Genesis 27:21-31