Genesis 27:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anasendera kwa Isake atate wace, ndipo anamyambasa nati, Mau ndi mau a Yakobo, koma manja ndi manja a Esau.

Genesis 27

Genesis 27:13-31