Genesis 27:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rebeka anatenga zobvala zokoma za Esau, mwana wace wamkuru zinali m'nyumba, nabveka nazo Yakobo mwana wace wamng'ono;

Genesis 27

Genesis 27:13-25