Genesis 26:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali atakhala komwe masiku ambiri, Abimeleke mfumu ya Afilisti, anayang'ana kunja kwa zenera, napenya, taona, Isake analinkuseka ndi Rebeka mkazi wace.

Genesis 26

Genesis 26:3-16