Genesis 26:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali tsiku lomwelo anyamata ace a Isake anadza namuuza iye za citsime cimene anakumba, nati kwa iye, Tapeza madzi.

Genesis 26

Genesis 26:23-35