Genesis 26:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti usaticitire ife zoipa, pakuti sitidakhudza iwe, sitidakucirira kanthu koma kabwino ndiko, ndipo takulola umuke ndi mtendere; ndiwe tsopano wodalitsidwa ndi Yehova.

Genesis 26

Genesis 26:23-35