Genesis 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kwa ana a akazi ace ang'ono amene Abrahamu anali nao Abrahamu anapatsa mphatso, nawacotsa iwo kwa Isake mwana wace, akali ndi moyo, kuti anke kum'mawa, ku dziko la kum'mawa.

Genesis 25

Genesis 25:3-14