Genesis 25:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Isake anali wa zaka makumi anai pamene anakwata Rebeka, mwana wamkazi wa Betuele Msuriya wa ku Padanaramu, mlongo wace wa Labani Msuriya.

Genesis 25

Genesis 25:12-27