Genesis 25:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zaka za moyo wa Ismayeli ndi izi: zaka zana limodzi kudza makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri: ndipo iye anamwalira, natengedwa akhale ndi a mtundu wace.

Genesis 25

Genesis 25:10-27