Genesis 24:65 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa mnyamata, Munthuyo ndani amene ayenda m'munda kukomana ndi ife? Mnyamatayo ndipo anati, Uyo ndi mbuyanga: cifukwa cace namwali anatenga cophimba cace nadziphimba.

Genesis 24

Genesis 24:55-67