Genesis 24:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye mnyamatayo, Kapena sadzafuna mkaziyo kunditsata ine ku dziko lino: kodi ndikambwezerenso mwana wanu kudziko komwe mwacokera inu?

Genesis 24

Genesis 24:4-7