Genesis 24:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthuyo ndipo analowa m'nyumba, namasula ngamila, napatsa ngamila maudzu ndi cakudya, ndi madzi akusamba mapazi ace ndi mapazi a iwo amene anali naye.

Genesis 24

Genesis 24:26-40