Genesis 24:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali, asanathe kunena, taonani, anaturuka Rebeka, amene anambala Betuele, mwana wamwamuna wa Milika, mkazi wa Nahori mphwace wa Abrahamu, ndi mtsuko wace paphewa pace.

Genesis 24

Genesis 24:9-19