Genesis 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu anati kwa anyamata ace, Khalani kuno ndi buru, ine ndi mwanayu tinka uko, ndipo tikapemphera ndi kubweranso kwa inu.

Genesis 22

Genesis 22:1-7