Genesis 22:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga anati, Usaike dzanja lako pa mwana, usamcitire iye kanthu; cifukwa tsopano ndidziwa kuti iwe umuopa Mulungu, pakuti sunandikanize ine mwana wako, mwana wako wayekha.

Genesis 22

Genesis 22:10-15